2026-04-21

Oyimba Otchuka Asangalasa Andende ya Maula

0
IMG-20230402-WA0103

Ndende ya maula, muzinda wa Lilongwe inadzadza ndi chimwemwe pamene oyimba awiri otchuka m’dziko muno Nepman Komanso Malceba anachititsa mphwando lamaimbidwe pa ndendeyi.

Poyambilira pa zonse, oyimbawa anapereka katundu okwana 600 sauzande kwacha.

Poyakhulapo, Smart Banda (Malceba), Anathokoza woyendetsa zinthu pa ndendeyi powalandira bwino komanso anthu akufuna kwabwino omwe anathandiza pazochitikazo.

Mwa zinthu zina zomwe zinaperekedwa ndi monga; Sugar, Sopo komanso ovala.

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *