2026-04-16

DDP yachotsa mayi Ganda ngati mkulu woyang’anira za chinsankho

0
IMG-20240910-WA0044

 

Chipani Cha Democratic Progressive (DPP) chachitsa mphungu wa mdera la Nsanje Lalanje a Gladys Ganda pa mpando wa mkulu wong’anira za chinsankho mchipanichi ndipo awapatsa udindo wina ngati mlangizi wa mtsongoleri wachipichi.

Izi ndi malingana ndi chikalata chomwe chipanichi chatulutsa ndipo chasainidwa ndi ofalitsa nkhani mchanichi a Shadreck Namalomba.

“Chipani Cha Democratic Progressive (DPP) chikulengeze kusithidwa kwa udindo kwa Mayi Gladys Ganda omwe anali mkulu wong’anira za chinsankho ndipo pano asankhidwa kukhala modzi mwa alangizi a mtsongoleri wachipani.”

Izi zikudza patangodutsa tsiku limodzi pomwe mayi Gladys Ganda anali nawo pa msonkhano omwe mtsongoli wa dziko lino Lazarus Chakwera anachititsa boma la Chikwawa.

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *