• Sat. Nov 1st, 2025

A Kanyenda akuti ayima nawo ku Sulom

ByStaff Reporter

Feb 20, 2023


Wolemba: Vitumbiko Mvula……..

David kanyenda walengeza kuti ayima paudindo wa-wachiwiri kwa mtsogoleli wabungwe la Super League of Malawi (SULOM) pazisakho zomwe zubwelazi osati paudindo wachiwiri wa mlembi wamkulu wabungweli.

Izi zadza pomwe ndandanda womwe bungwe loyendetsa zisakho za super League latulutsa likuwonetsa a David kanyenda pamaudindo awiri, wa-wachiwiri kwa mlembi wamkulu komanso wachiwiri kwa mtsogoleli wabungweli.

Iwo apempha anthu omwe anawasankha paudindo wachiwiri kwa mlembi wamkulu kuti asawasiye koma akhale nawobe paudindo umene ayimilewu.

Ndipo a Kanyenda apikisana ndi Col Gilbert Mitawa pa udindo wachiwiri Kwa mtsogoleli pa zisankho za SULOM zomwe zili pa 25 February 2023 Ku mangochi.

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *